audio
stringlengths
43
45
text
stringlengths
0
24.1k
start_time
int64
0
1.83k
end_time
float64
1.74
1.85k
./data/chichewa-dataset\audio\segment_601.wav
Okay ah komabe mumachita bho. sinakha kuti muthu uziwerenga komanso kuti uzipanga ndi izizi sizimagwirizana iai.
0
7.594688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_602.wav
Okay ndiye mawa bwanji sizingatheke saturday?
0
3.328
./data/chichewa-dataset\audio\segment_603.wav
Lero sizingatheke ndili busy ndili busy. litakhala monday kapena lachiwiri kapena sunday.
0
8.618688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_604.wav
Okay ndimafunsa kuti mumafuna kuti ndizabwere mkoko? kuma hostel kwanuko.
0
6.485375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_605.wav
Okay ukutanthauza kuti ndizabwere kumenekoko? ndiye ndikufunsa.
0
4.693375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_606.wav
Tayankhulani chichewatu tikupangeni Mom Dad on the car Tayakhulani Tayakhulani chichewa Mukuzikakamiziranji? Ah Kuzikakamiza
0
18.599188
./data/chichewa-dataset\audio\segment_607.wav
Eetu aise koma aaa mpata ukapezeka leloro unakakhala kuti unalipo ndizotheka ndinakadya koma nanga si iwenso mpatawo? kodi iweyo umakhala mbali yake iti?
0
13.141375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_608.wav
Okay aise undiuza, undiuza. ine malo mu Blantyre ndimatha kudziwa kuti mu Blantyre koma nanga ndimakhala ku Chilimba Ndiye nanga ndiganene kuti tikakumana malo akuti? ine ndimadziwa kuti malo ambili ndi kuchiii.... and ndinakumana ndi ada ena ake akandiuza kuti tikakumane nawo kwakuti. ndinawauza kuti sindimapanga zachibwana. sindigamapite ku room yii azikandiona athu azikati mwakuti. Sindinapangepo chibadwireni changa
0
24.490688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_609.wav
Ndiye ndi ya wani week yokhatu nanga apapa ana atsala ndi 4 weeks. ndiye 4 weeks tikachotsapo week inoyi tatsala ndi 3. Pa 3 ndiye kuti ah nthawinso yolemba mayesoso. ndiye kuti ikhala one week survey yaketu. ndiye kuti 5 schools 5 schools 5 schools 5 schools. Eh kaya panja ndi unjeni ndi chani? ndichani panja? uh ndiye eh ndi IPOR. a Mazy tangoona alemba chibaluwa chawo pamenepo. Chachikulu.
0
26.965375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_610.wav
Ah unjeni of course ndi pilot chabe ndiye agotenga ma guy achina Prince kaya ndi athu 5 kaya. eh agopanga pilot sinanga unjeni eti akuti asitha ma tools. like ah mukavaya pa geli panja, kukhala ngati achina mothergroup anja chanichani zimene zinja azichotsa Ndiyeno akufuna angoyesa apapa lero ndi mawa. Angoyesa kuti ngini ikuyenda bwanji. Then i think ayamba kuimba ma phone kuti tikapange mwina ma refresher training chanichani. Eetu sinanga simensa MESIP ya apapa yii ikhala yaifupi kwambili. Sample ndi yochepa
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_611.wav
30
36.778688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_612.wav
Ah ali bho athu amene awatenga MESIP woo apite MESIP yoo amenewo. akapange pilot. koma kwatsala 4 weeks yokha kuti ana atsekere school
0
10.069375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_613.wav
Ndinakumana naye dzulo ndiye sitinapange exchange ma namabala. Ndinakumana nacho dzulo. Eetu kaya akuzatani kaya ku Zomba kuno?
0
11.776
./data/chichewa-dataset\audio\segment_614.wav
Yesi bwana Matekenya!, ha bwana ine basitu ndimagofuna ndikukumbutseni tikumbutsane za pempho linja ndinakupemphani abwana. (waipeza?) pa pempho ndinakupephani abwana ndimafuna ndikukumbutseni kuti chonde abwana mbale wanga muesetse mundiyesetsere ndithu kutinso munandiuza kuti ah komano mwenzi wa mawa wa Malichi wo ndiye panopa ndimafuna ndithandize kaye ena ndiye mwenzi wa mawa ndikuthandizani. Ndiye abwana ndafuna kuti ndikukumbutseni chonde bale wanga. Mundiyesetsere mwa Ambuye kuti mundithandize inuyo abwana. Ndithu, ndithu mbale moni kwa alamu ndi anawo. Zikomo apanso foni ndikusiyana nayo foni zobwereka izi. Ndithu mbale.
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_615.wav
30
51.285375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_616.wav
Iii nambala ya Robert ndilibe. phone kusitha-kusitha basi tinataya nambala ya a Robert.
0
8.448
./data/chichewa-dataset\audio\segment_617.wav
Ah aise Rich ugule nambala ya TNM mwamva! Airtel yakoyi ah ife timakonda TNM. Tangulani TNM tizikuiimbilani.
0
9.898688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_618.wav
Kodi Rich kodi bwanji aise eh bwera. bwera kukhala ngati lero wadzuka mwa unjeni mwa libido eti ukufuna ukhale father wa Libido?
0
11.434688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_619.wav
Uwapatse moni akazako. wamva? akazako uwapatse moni. ufiketu moniyo?
0
8.789375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_620.wav
Ahaha inuyo munamwa mumamwa mwa mpikisano? simafunika kumamwa za mpikisanotu zimenezo. Ndiye pulasi kaunjeni unatenga unja special. Ah a Rich simumadziwa kuti timakhala mu Zomba nthawi yoseyi? Zomba aise Matawale.
0
18.688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_621.wav
Uh mh sinadzuke bho. Nthobwa lakuchikhoswe landitsegula mimba. Ee aise uli kuuu kuti? ku Balaka or kuuuu tanena bwinobwino.
0
13.568
./data/chichewa-dataset\audio\segment_622.wav
Eh a Richi! bho bho. mwadzuka bwinotu lero.
0
7.082688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_623.wav
Bho?
0
1.792
./data/chichewa-dataset\audio\segment_624.wav
Azathu a chamba dzukanitu. Dzukani kwacha. Ife tikuvaya kuma dis amwene.
0
8.362688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_625.wav
Timangolowa aise Phalombe, Phalombe. Iya Phalombe, Phalombe amwene zamafuta anatiletsa. Ndiyeso ndizivala zimene zinja mafuta iai-iai.tidwalatu hihihihi. iii aise ndikuona mawa ndatopa ndigone. Mawa tili ndi ma dis ndiye ndikukapanga lead ndiineyo. Ndakuuza kale uzabwereko pa Bananapa. eee kuchokera kumeneko kufika pa Banana kaya i think ndi 2 hazi olo 3 hazi. ndi pafupi
0
25.685375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_626.wav
Wana Dasitani ndine Antony Chikanda abwana. Ndimati mukhale pa laini kuti tiyakhulane. Ndithu mbale wanga
0
14.08
./data/chichewa-dataset\audio\segment_627.wav
Aise ndiye umagolowa mutu-mutu? ah ubwino wake uli ku chipatala uma...umangotenga zokumwa. Okay basi ife ma daso aise koma opandapo mowa eti. wakamva kameneko? bweratu! ubweretse watsalawo. hihihihih
0
19.370688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_628.wav
Hihihih ahaha mwana! hahah zachibwana basi. Mwana iai zitayeni. za anazo ayi. anawo mwabereka inuyo akwanira basi. akwanamo dziko muno. Kondomusotu ayi anatiletsa zamafuta. Zamafuta anatiletsa ife ndiye kondomu sitimavala.
0
21.333375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_629.wav
Hhihihih man! muzakakwatira muzakhala ndi mwana amene azakhale wanu. Chifanizo chanu. Waiona? aise nanga uzigothila pa bed ee basi, basi pa bed ndi mkondomu. Ah iai tatulutsani nkhope yanu.
0
18.005375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_630.wav
Ah ah kusandikonda ndiye kumeneko. Munakakhala kuti mumatikonda simungatiuze zokwatila amwene aaa. Mumatikonda zenizeni inu? Mutiuzilanji zokwatira? ah uzakwatire ineyo? hahahahah tikondeni amwene tiuzeni zina koma osati zokwatira.
0
19.029375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_631.wav
Hhahahahaha aise! advisor wako ndani amene amakulangiza zamahule? eee? aise inetu ndimalangiza zithu zabwinozabwino zokhazokhatu zokuti uzakwatire, uzakhale ndi mkazi modzi. waiona!uzakhale mkulu wa mpingo. waona. ndimalangiza zabwino zokhazokha positive.
0
17.152
./data/chichewa-dataset\audio\segment_632.wav
Ah koma Mulungu sangandipatseko amzanga abwino? kungondipatsa zingawenga zokhazokha. Sangandipatseko mzanga wina wake oti azindilangiza? azindiuza ma verse. Kungondipatsa ma hule basi. zidakhwa. iyaa.
0
15.445375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_633.wav
Iwe ndi wampingo wanji? hihihih
0
3.157375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_634.wav
Ndakutulukirani hihihih anyamata a libido. Nonse amene munali busy kukomenta mmene munja mkati munja ndimakuonanitu. Ndimadziwa kuti anyamata a libido awa. Achina Allan. iiiiii koma guys. Aise mawa ndizagofika ndifika ndikufuna ndizagokuona basi. Ndizagokuona kenako ndizavaye ku deni. Ndikufuna ndizakumanenso ndi mkazi wina wake akupanga SNE. Wina wake kakafupi koyera kokongola ndikufuna ndikagokumana nako basi. Kenako ukudziwa kale. Ugone bho ndikufuna ndizigona apa.
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_635.wav
30
39.082688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_636.wav
Hhihihihi Aise ine ndi wamtali aise hihihihih koma inu iiii eee athu afupiafupi amwene zimakhala kuti zimichira zanu zazitali ati msinkhu umakhala kuti unathawila malo amodzi. Ndiye kumenekoko, Mumalilitsa nazo azikazi. Azanu akoka dzulo. Mkazi kumagokuwa kuseliku Ah akumafika nawo pati kaya
0
23.637375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_637.wav
Kodi ukuti watani walakwa chani Kelvin? Wakutaa! Akuvutitsa Akuvutitsa? Uh Wavutitsa chani? Usandivutitse uone! Oh Ndikukuzatu ndikatenga chikwapu Akukatenga chikwapu chinja Akukatenga chikwapu? Uh Ayi sakumenya. Usaike mkamwa Bukhu uh
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_638.wav
30
42.048
./data/chichewa-dataset\audio\segment_639.wav
Hahahaha Eh eh wtokotatu aise. Kodi athu afupiafupi mumadziwa kunyenga, umadziwa? kodi umazitenga kuti ndiwe wamtali kapena wamfupi? iwe ndi ine chimodzimodzi basi. Ah man tatiyeni tizigomwa mowa.
0
13.397375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_640.wav
Ah amwene zonyenga zisiyeni. Zonyengeratu amzanu chipinda cha ukocho anyengana anakoka anyenga basi. Ife kutisiya kuno iwo kumanyenga uko. Ndiye chimkazi chake chimagolira ife kumamva kuno. Zachibwana. Basi ndasiya. Pa getipo ndizigosiya Agalu zi akazizo sizimabwera. Muzinyenga komweko uko ku balako kunoko mukamabwera mutanyenga kale. Muzingosamba basi iyaaaa.
0
26.453375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_641.wav
Ah man inuyo mugotsegula nyumba yanuyo kuti athu tikafuna kunyenga tizibwera kuzanyenga kumeneko basi. Sikuti muzibwera ku mowa osanyenga basi muzizanamizila kugona pamenepo mutanyenga kuseli kwa bala ku unjeni kwa kauta. Ee kukhala kwa bwanji kumeneko? Tapangani tizi... tizi hihihihihih
0
20.309375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_642.wav
Amwene mavuto amwene iii azanga aine ndawatenga amagona kunoko eti. of course timagona limodzi ndi Kelvin. Wandemvu zake uja. Zonse za Ndemvu zimagona kunoko zimandipatsa busy ndi ndemvu zaozo. apa tagopita ku village basi. Ati agona komweko anyenge Hihih ihih iii guys.
0
20.48
./data/chichewa-dataset\audio\segment_643.wav
Kodi ukumwa chani? Castel? kapena Chill? kapena kachasu
0
5.632
./data/chichewa-dataset\audio\segment_644.wav
Alright thanks a Shad kugoti ee aise maluzi atikwapula. i am really broke,broke. mwenzi watha koma ndilibe kalikonse aise. Kalikese ndilibe aise
0
15.018688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_645.wav
Pa gulupu pano ndiku……muli ndi chibwana
0
4.245375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_646.wav
Bwanji uyu wotsongolera Anti-corruption bureau. Ameneyu asamasankhidwe ndi presidenti chifukwa ambiri amakonda kulakhula mau akuti munthu saluma chala chimene chikumdyetsa amatero wanthu Mm inu mudzalola kuti mphamvu imeneyi,mutakhala presidenti musakhale nayo yosanlhaa…. Ndinje kusintha maganizo anga. Zimene zinja tinafuna ife mbali yotsutsa ndi zimene tidalakhula manifesto yathu zimene tikuyakhula manifesto yathu koma vuto lake azanthuwa adalakhula manifesto yathu amamchita chimphimba maso. Monga zimene akulonjeza masiku anozi, chimphimba maa…. Kungophimba maso a Malawi koma ndikudziwa kuti amalawi azindikira tsopano kuti ‘ Ah ili ndi bodza la nkhunguniza’ Chimphimba maso? Ah ndithu, chimba maso. Alibe mtima woti akhoza kulimbana ndi katangale. wakanika zaka 5. Kukanikilatu. Kuba lero ndiye kwapita mtundu wonse pamwamba. Katangale ndiye wafalikira paliponse. Koma zolankhula zabwino zedi. ‘ah tithana ndi katangale’. Mm Iyayi simawu okhayi, koma ntchito zionetse
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_647.wav
30
60
./data/chichewa-dataset\audio\segment_648.wav
60
71.125375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_649.wav
Hallo? Yeah yes madala. Yes madala mwaswera? Ndaswera bwino kaya inu? Ah taswera. Ndaona unjeni ah website yanu Uh uh Ah wina wake mzanga ananditumizira Uh Eh ndiye ndimaiona going through kupeza kuti ah introduction ya on herbals ikupezeka kuti exactry reeflet yanga kuti ah zikukhala bwanji? Iayi sitinapangeyi Simunataa? Sitina ….. anagokopera ah Uh wakoperatu word for word chilichose pa leaflet yonse Tadikira kaye anangokopera ah pa pa profile Eh Sinakhale operational Eetu Eh tikusitha tikuchotsapo zimenezozo. Eh ndiye ndaona mwambiri kuti ah mwagokoperatu exactry za azanu simunalembe zanu bwino-bwino? Unjeni olo ma products ma label woo kupezeka kuti moto yoo mukuyusa ya ife kuti ‘quality archived. Safe guarateed’ ife mmene timakalembetsa kumeneko anatifunsa kuti mmene timakalembetsa campany kuti; ‘moto wanu ndi chani?’ thus the registered trademark. Tinachita kuinganiza sikuti tinakopera pa ena ake iai. Mwaona? Ndiye kuti tizipangana kuti inuyo ndi azanthu eti? Ndiye kuti tizipangana pakana ma lawyer alowerere. Awa akuyusa zithu zathu chani, chani siza bho. Tagopangani Ayi sizabwino Muzipanga koma muzipanga zanu Tikaimaliza tikuonetsani muiona sanamalize ndi komwe. Ma label mupange anu bwino-bwino sikuti timaletsayi. Business yathu aliyense kumapanga modzimodzi sikuti mumapanga munthu mmodzi basi zii ayi. Olo maunjeni mankhwala kumapezeka kuti kuli unjeni ketamu famanova aliyese amapanga kaya zofanana koma aliyense mwina akuyusa ma unjeni ma kalazi ake, ma unjeni info yake chani, chani like that Uh eetu inunso muzipanga koma kugoyusa zanu bwino-bwino. Okay tikuonetsani tikamaliza bwinobwino Chirwa tikamaliza ineyo ndikuonetsani sinapange chinachilichose Athuwa ndi omwewa ndi andani Eya Okay I was just concered ndi zimenezozo last time tinanenanso chocho kuti ah ma products timakungulitsani kuti inuyo muzigulitsa kumachotsa ma label mkuika anu. Ndiye muike bwinobwino musaonekeretu kuti mwachita kutenga za ifeyo. Okay Eh tiku… Tikonza Tinakazayamba kumakana kuti ‘ah sitikupangirani ma capsules chizakhala ngati chipongwetu. eh inuyo ndi zathu tangopangani inuyo mukamatigula mukapapititsa kwa anthu mukutipangiranso market soo. eh eya komano zizioneka kuti ndi zosiyana awa ndi ena awa ndi ena zisamachite kuoneka kuti ngati tisapapange confuse ngati ma copy kazi iai okay ndikuuzani ndikamaliza zonse alright thanks for it yeah sure
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_650.wav
30
60
./data/chichewa-dataset\audio\segment_651.wav
60
90
./data/chichewa-dataset\audio\segment_652.wav
90
120
./data/chichewa-dataset\audio\segment_653.wav
120
150
./data/chichewa-dataset\audio\segment_654.wav
150
178.816
./data/chichewa-dataset\audio\segment_655.wav
Ku 24, 23 kumaoneka chochi. 24 ndiku 23 eh anthu aku 24 ndi 23 kwanu kumaoneka chochi. Ayi ndithu. Ndiye mumadutsa pati
0
19.876313
./data/chichewa-dataset\audio\segment_656.wav
Komanso zimene ndisakusangalatsidwa nazo ndi chonena kuti, munthu pulizitu mundivetsetse!. Mundivetsetse. Sindikufuna kuti musamutenge iai koma inuyo mundivetsetse. Ineyo munthu sindikumudziwa sinamuonepo. Mukundivetsa eti?. Koma mavuto aku Malawi ndimawadziwa chifukwa ndabadwira mkoko ndakulira mkoko and munthu akamandipempha kuti ‘ayinse ndikufuna ndibwere ku south Africa even ineyo ndisakumudziwa ndimamuthandiza. Mukumvetsa? Ndimamuthandiza munthu oti sindikumudziwa. Ndimamuthandiza bwino-bwino. Ndiye ineyo ndikuyakhula ndi makolo ake. Mukuona? Makolo ake ndikuwauza kuti ‘musadandaule ndimutenga’ ndiyeno ndikuwauza kuti tapangani zakuti-zakuti-zakuti anja sakundiuza zoona ineyo ndikumapanga madongosolo Osaka-saka ma transporter osakasaka kuti ndilipile transport ah iwo mwana wawo alibe passport iwo osandiuza kunena kuti mwana wathu alibe passport. Iwowo eti ndikumandiuza molimba mtima kumanena kuti; ‘panopa mwana ali ndi passport’ alibe passport. Ndi ndalama zingati zimene timalipira tikachoka munthu akakhala kuti wabwera opanda passport kufika pa bert-bridge panja ndi ndalama zingati zimene timalipira munthu akathawidwa? Eh! Amapanga chocho? Ayi inu zimenezo sizikundisangalatsa zimenezo. Zimenezo sizikundisangalatsa iyayi. Mwandimvetsa? Sindikunena kuti ineyo sindikufuna kumutenga iai. Ineyo ndikhoza kumutenga bwinobwino mwanayo kumabwera kunoko. Zoona. Chabwino ngati iyeyo akuyendetsa chinyamata inu makolo achewo akuyendetsa chinyamata? Munthu alibe passport alibe chinachilichose alibe passport akufuna kubwera kunoku ku south Africa. Ine ndikupanga madongoloso a transport pozindikira kunena kuti munthu amene akufuna kubwerayo akuti passport alinayo koma transport alibe. Ndikupanga madongoso a chani a transport kuti ndimuthandize abwere kunoko. Ndikumandiuza kuti passport ilipo ndamuuza kuti ‘tatenga passport yako upite kwa wakuti’ munthu unja osapitako akudziwa kunena kuti alibe passport. Kodi amaganiza kuti ndimuuza kuti asabwere kuno? Amapanga chocho? Olo nthawi zina ndikamakhala ndikuwalongosolera anthu ena ache aziti bwanji? Ndikuwauza abale anga kokuno ku south Africa amene ndimakhala nawo kokuno koma madera ena. Akuvutika akusowa chani, akusowa ntchito. Ine ndapeza mwayi wantchito ndikusiya kumutenga mbale wanga woti wafika kale ali kokuno, daily amatani, amandi….amaaa amandifunsa; ‘akolo ntchito kumeneko mukamvera mundiuze. Ine kuno ndikugokhala’ eh ‘ndikugokhala ndithu ntchito…’ ali mu south Africa momuno. Ndiye ndikupanga ma pogram oti munthu ali ku Malawi koma sindikumudziwa sindinamuonepo palibe chibale china chilichose ndikumutenga kuti atani abwere kunoko ndikukamapanga zimenezi? Olo makolo akewo akudziwa kuti mwana wangayu alibe chani alibe ine chimene ndinadabwa nacho makolo ake onena kuti mmene ndimawauza kuti ‘bwerekani ndalama mwenzi ukatha ine ndilipila ndibweza ndalamayo. Simwati mwana ali ndi passport? Abwere kunoko basi’. Makolo ake osandiuza kuti mwana alibe passport. Oti ndinakatenga ndalama ndikuwatumizira makolo akewo mu phone mwawomo ndikuwatumizira ndalama kunena kuti ndalama imeneyi mpatseni mwana wanuyi azibwera kunoko ku south Africa. Akanampatsa kuti akakwere galimoto azibwera kunoko kapena bwenzi akukapanga passport? Chabwino. Anakakhala kuti ndalama ndalama ndatumiza ndiye apanga passport. Ndiye transport anakapanga ndaa? Anakapanga okha? Amapanga chocho? Ee pepani. Auzeni kuti ndasamba m’manja.
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_657.wav
30
60
./data/chichewa-dataset\audio\segment_658.wav
60
90
./data/chichewa-dataset\audio\segment_659.wav
90
120
./data/chichewa-dataset\audio\segment_660.wav
120
150
./data/chichewa-dataset\audio\segment_661.wav
150
180
./data/chichewa-dataset\audio\segment_662.wav
180
205.524
./data/chichewa-dataset\audio\segment_663.wav
Amkolo kumeneko ntchito anampezera kale ndipo mzunguyo amene atakagwire ntchitoyo tayakhula naye Benard yoo ndipo akumuuza kuti nthawi inailiyonse anganyamuke pa mwenzi uno ntchito akayamba akudikira iyeyo. Ndiye ah za kolonazo tinaesera kufotokoza koma iyeyo wanena kuti ayi apitebe ndithu za kolona m’boza zakutinso akhoza kusiya chifukwa cha kolona wanena kuti leronso tayakhula naye mzungu ndi mzungu sikuti ndi mwenyeso ndi mzungu. Mzungu ndi mzungu sikuti ndi mwenye. Ndithu amkolo ndi chifukwa chache tikuchita sawasawa kuti ah nanga zithu zoterezi zilepherekenso azanga? Ukapeza kuti mwina tayamba kukapezako kakagomiya tayamba kumangapo pa ntchaya ndikufundako ndithu. Eetu amkolo kuti mwina ndiponso kuti zopephapephanzi ine sikwenikweni ayi. Mwinanso mukhoza kudabwa kuti angalephere bwanji amalume anga. Ndithu amkolo
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_664.wav
30
57.3
./data/chichewa-dataset\audio\segment_665.wav
Ah Amkolo ndinanena kuti ndimagwira kanganyu kwa Bodwe ndiye ndimagulitsa mu gulosale mwawo ndiye mudziwa January yuu ka golosale atseka. Ndiye sizikuyenda. Ndiye apapa pali chipwilikiti ndimafunako Kandalama chithandizo kuti ndiyambileko kabisiznesi town muno. Ndisafala ni wana ndiye ndikhala bwanji town ndi wana munditumizireko kandalama amkolo chonde, chonde
0
24.617375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_666.wav
Ayise, ayise machine amene ndimakuuza ndi amenewa Ada. Ndi amene ndimaku ndimakuuza. Ndiye mwina zitatero kuti ngati zingakhale zotheka kuti mbale wanga ungomugulira amenewa basi
0
14.121375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_667.wav
Abwera awa? Ee ndibwera ndi mmene timakhuthulira….. Mwawaonetsa mwala uwowo? Ee sir ichi Ichi, ichi chimwalachi cha uku mwauna direct mwala uwo? Miyala iyi ili ukuyi Ili ukukuyi? Ee Ayi safika kwinakuyi yofunika kuinyamula eh abwera awa? Eh kubwerera ibwelera koma ima…….
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_668.wav
30
38.761375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_669.wav
Abwera awa? Ee ndibwera ndi mmene timakhuthulira….. Mwawaonetsa mwala uwowo? Ee sir ichi Ichi, ichi chimwalachi cha uku mwauna direct mwala uwo? Miyala iyi ili ukuyi Ili ukukuyi? Ee Ayi safika kwinakuyi yofunika kuinyamula eh abwera awa? Eh kubwerera ibwelera koma ima…….
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_670.wav
30
35.412
./data/chichewa-dataset\audio\segment_671.wav
Hallo amkolo ndine Amon, Amon, Amon Chandawira. Kodi malume munatitaya chocho chifukwa chani malume tazanu. Kunoko sitikugwira timaganyutu. Ndimafuna amkolo tiyambeko ka business kenakake mwina kogulitsa Chimanga cha Nsima. Mutitumizireko pang’ono tazanu ndili kuno ku Mzuzu kumudzi sindinapite iai. Pakati apa ndithu ndinali kwa Bondwe ndiamene penapake amatithandizako koma mpopanonso kaganyu tatani, tasiya moti tingokhala tawuni. Malume chonde, chonde. Kaya mutumiza kaya ndi ka 50 sauzande kaya palibe kathu. Kogoyambira business yoo basi. Zikomo malume
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_672.wav
30
35.22
./data/chichewa-dataset\audio\segment_673.wav
Ah Amkolo ndinanena kuti; ndimagwira kaganyu kwa Bondwe ndiye ndimagulitsa mu golosale mwawo ndiye mukudziwa January yuu kagolosale atseka. Zithu sizikuyenda. Ndiye apapa pali chipwilikiti. Ndimafunako ka ndalama chithandizo kuti ndiyambileko business mtawunimu muno. Ndisafala ni wana nanga ndipanga nawo bwanji wana? Munditumizireko kandalama amkolo chonde, chonde
0
24.617375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_674.wav
Hallo Amkolo, ndiye mwati vuto ndi chani? Sindinamve chilichonse ine! Pakakhala vuto ine Asante amandi…. amandiuza ndiye sanandiuzeko chilichonse
0
15.7
./data/chichewa-dataset\audio\segment_675.wav
Nkhani iyiyi nkhani iyiyi nawonso ankhala ngati kuti alowa maganizo mwathu. Kuteloko tikubwer ku maliro a Getu kuja tikakambilananso mgalimoto. Timanena kuti tikafika, tii tipeza kanthawi yoti anthu akumudzi anja asanapite, tikhale pansi tiiikambilane patalipatali. Ifenso tinapangadi chimenechocho kuti iwowo akonze njerwa oumba, oumba panja alipo zapang’ono ifeyo akutali tikoza simenti ndipo ndi zoonadi. Ifenso tina…. Tinakambilanso zimenezozo mu galimoto. Ndiye tinagwirizana kuti tizisonkha ndalama azisunga ndi Nema. Azisunga ndi Nema ndiye timaa ndi mmene mwaneneramu kuti zitha chaka cha mawa, ndinkhani yabwinodi kuti tiyambila patali. Panopa nthumba la simenti sindikudziwa kuti zikumatengera madera kuti ndi ndalama zingati. Koma ndi yosafika 10 sauzande. Mwina 7, 8. Ena 6 imene. Zimagotengera kuti ndi kutiko. Ndiye maganizo anga ndi onena kuti; sindikudziwa kuti tipanga bwanji. Ndimanena kuti ka ndalama ngati kangachepe tiyambe kusonkha pano. Tizimutumizira Nema kaya pa nambala ya airtel money popeza ndi imene ili change-changu. Pa mwenzi tizitumiza mmene munthu wapezera. Kaya 200 kaya atumiza 100 kaya 500 kaya 1000. Ndi mmene munthu watani, wakonzera. Ineyo ndimaganiza chocho. Sindikudziwa kuti anthu maganizo anu akhala otani. Or maganizo ena, popeza munthu ndi munthube, olo titanena 100 tipezeka kuti pali anthu ena 100 osatani, osapereka. Poti mwanena kuti zilizazo zifunika 9. Zipangidwa 9. Ndiye ndimaona ngati kuti tinakapeza anthu ozidziwa ozitsata bwino, paziliza 9. Akwana mitumba angati a simenti. Tinakapeza kuti ndi angati, ndiye popeza kuti ndi chaka cha mawa chaka chino ngati simenti ili 8 sauzande. Ndiye potin di chaka cha mawa. Tikhoza kuuika mwina pa 9 sauzande. Ndie tipeza matumba 9 woo ndi ndalamayo kuti zikwana ndalama zingati. Ndiye tikaipeza ndalama inja. Ineyo maganizo ena. Tikaipeza amount inja. Ndiye tizitanino tiyamba kusunga ndalama zanthu zinja kuti aliyense azipereka mwenzi uwu mwenzi wantha tikhoza kupangana kuti ayi chabwino mwenzi uno tiyeni tiyesese mwina ya nthumba limodzi kapena yamatumba awiri kapena ya nthumba limodzi ndi half. Mwenzi wamawaso, chocho poti chaka cha mawa ndi kutali. Ndikukhulupiliranso kuti nanenso chaka chamawa izakhala nthawi yamvula izakhalanso mwina ngati nthawi ngati inoyo. Yoti athu muone kuti anthu akolola. Eetu maganizo anga ndi amenewowo. Ndiye palinso athu ena muna aziadimini inuyo muyang’ane ma contacts anuwo amene li a chibale athu koma apapa palibe. Koma mu contacts mwanumo alimo. Muwapange add. Ifenso tifufuzafufuza mafoni mwathumu. Amene ali achibale koma apapa palibe tipeza nambala yoti apapa muwapange add. Atleast nkhani iyiyi tikambilane. Ineyo maganizo anga ndi amenewowo. Muuzenso anthu ena.
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_676.wav
30
60
./data/chichewa-dataset\audio\segment_677.wav
60
90
./data/chichewa-dataset\audio\segment_678.wav
90
120
./data/chichewa-dataset\audio\segment_679.wav
120
150
./data/chichewa-dataset\audio\segment_680.wav
150
180
./data/chichewa-dataset\audio\segment_681.wav
180
191.721375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_682.wav
Amkolo muli bwanji? A Matekenya. Ndine Amon Chandawira kuno ku Mzuzu. Tati tikupatseni moni. Komanso tikufuna tikufotokozereni kuti aeni ake a foniyi nawonso ndi amisili ndimanena anja. Moti akudikiratu ulendo wakuzomba kuti uli pati? Ndithu Amkolotu. Ndiye mmene zililimo muzitifotokozera. Zikomo.
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_683.wav
30
31.892
./data/chichewa-dataset\audio\segment_684.wav
Hallo amkolo ndine Amon, Amon, Amon Chandawira. Kodi malume munatitaya chocho chifukwa chani malume tazanu. Kunoko sitikugwira timaganyutu. Ndimafuna amkolo tiyambeko ka business kenakake mwina kogulitsa Chimanga cha Nsima. Mutitumizireko pang’ono tazanu ndili kuno ku Mzuzu kumudzi sindinapite iai. Pakati apa ndithu ndinali kwa Bondwe ndiamene penapake amatithandizako koma mpopanonso kaganyu tatani, tasiya moti tingokhala tawuni. Malume chonde, chonde. Kaya mutumiza kaya ndi ka 50 sauzande kaya palibe kathu. Kogoyambira business yoo basi. Zikomo malume
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_685.wav
30
35.22
./data/chichewa-dataset\audio\segment_686.wav
Iii koma ii koma koma ndi zabwinotu koma ii ayi the feeling kuti mwina board yathu amatipatsaa ndalama zochepa koma iii ndiye utenge chibenzi cha nyuwani chinja. Osagochitenga bwanji? Ah kumeneko ngati athu amapangapanga Ngozi? Palibe zoti ungagwe misewu yake yabwinobwino. Kungoyitenga. Iii ndinaona benzi ina yake mu…. Iiiii olo nditakhala ine ndikhoza kuitenga. Munakangotenga. Athu ake ndiyetu mpaka kukupatsani benzi akuona kuti galimoto ina ili ku service! Iii ee koma. Kuno ndi cash tuu. Cash, cash ndikachithu ka 500 000 komwe cash. Palibe zoti …… athu kunonso ndima khuluku sangamapange. Kaya mwina its automatic kuti ikangobwera umapanga. Koma ndaona unjeni, ndaona kapani ina yakenso koma ndiyama electronics. Komano sumatenga chithucho. Ndiye zoti umatenga koma its automatic. Once you have the money at the end of the every month, amaichotseratu okha mkoko. Koma ndiye kuti ….. its almost everything kaya ndi fridge ya 2 miliyoni. Amakuchotsa amachotsa. You agree percentage. Koma iii magalimoto I think athu angalore. Koma bola nyumba iiii ndimafoni omwe? Ah nyumba, nyumba mwina ndi galimoto its okay for me.
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_687.wav
30
60
./data/chichewa-dataset\audio\segment_688.wav
60
81.385375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_689.wav
Yeah pano tili ndi munthu yemwe anapezeka ku Ligoni amanena kuti wamwalira unja komano athu anagotenga mtembo wa eniake. Mwini wake weni-weni ndi uyuyu. Akulu tafotokozani bwinobwino Ah chimene chinachitika ndi choti ine ndinali ndili kwa Namatchowa ndikumwa mowa. Ndiye abale anga anagomupeza munthu wina wache atafa. Ati ndinafanana naye kwambiri koma sindinali ine iai. Ine ndinali ndikumwa mowa kwa matchuwanaku. Eetu koma muthuyo anapita ndima bulangeti anga, ID yanga zonse zinapita. Panopa chovala ndi chomwechi mukuchionachi basi
0
29.977
./data/chichewa-dataset\audio\segment_690.wav
Kumupeza kuti zimayi wadutsa, basi ‘ona mwendo, mwendo, mwendo; mwendo’ Hahahaha Ah moti mzoona zoti munthu amayenda miyendo zachilendo? Ayi Zachilendo? Nkhaniyi ndi chimasomaso
0
19.086813
./data/chichewa-dataset\audio\segment_691.wav
Ndiye ndiayimbile foni mwina
0
8.128
./data/chichewa-dataset\audio\segment_692.wav
Ah ndawapatsa koma akuti aitanitsa ati a Fyuzgo ndiye mwina afika kaya ma week ati kuchokera ku south africa. koma poti dzulolo imavuta ati mmene amachoka town imagoti phuphuphu ndiye akagoikabe awowo akudikira a fyuzgo woo kuti asafike
0
22.654688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_693.wav
Apa ndikubwerako ndimafuna ndikafikano ndiye tiyankhulane. apa tikuthamangira pa boarder ya pa Songwe. koma ma unjeni anja ndinagula ma pakate awiri koma ma pack awowo amakhala a excel amakhala 15, 15. Ndiye ndinawafunsa ngati ali ndi yotsegula kuti tiwone quality yake ndiye anati aah alibe yotsegula komanso awowo sangatsegule. ndiye ndinagula ma pack awiriwo ngati ma piece 30 oti aka.... unjeni tikawapatse apapa akayese kugwiritsa ntchito koma ndi angati makabudula. Ngati angakhale kuti akugwira bwino bwino weekend yii ndikapita ndiye kuti ndikagula onse otsalawo. koma awawa ndi ama.... akumakhalamo 15:15 sama 10:10 anjawo iai
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_694.wav
30
60
./data/chichewa-dataset\audio\segment_695.wav
60
65.172
./data/chichewa-dataset\audio\segment_696.wav
Ndiye awowo alipo ma pack awiri ndikujambulirani ndikutumizirani. Ndiye ndia... ndiwapatsira a head chifukwa ndili ndi a head ndiye kuti akawapatsira. Ndithu. ndiye mmene aneneremo ndiye kuti ndizigula type imeneyo. Ngati anganene kuti type imeneyo siyabwino ndiye kuti tisitha ndikatenge type ina. Koma vuto lake ndiloti sizithu zake panopo zandula ndiye tikugoyenera kuzivomereza basi
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_697.wav
30
33.556
./data/chichewa-dataset\audio\segment_698.wav
Okay ndiitanitse invoice mpopanopo
0
4.372
./data/chichewa-dataset\audio\segment_699.wav
Inu ndinu ndani chimwemwe Bwanali TNM call centre ee mukuti bwanji amwene? ee tinatumiza ma message mwenzi wathawu ehe eee okuti chani? okuti mupange sim-card update sim-card yanu sindikudziwa kuti ma message atabwera munapanga follow? ee ndinapanga kale update koma mu system mwathu simukuonetsa kuti munapanga update ndiye ngati sindinapange update bwanji phone ikugwira ntchito? nambala ikugwira ntchito? ndi chifukwa chake takuimbilani a kasitomala kuti mu system simukuonetsa kuti munapanga update. koma ndiye office yanuyo yaugalu ikugomveka phokoso ikakhala kuti muli mu office ohkonso limenelolo. wagoshota aise unakangonena kuti ukufuna zingati ndikuganizire basi. wamva? ndiwe mwana wang'no ukuyakhula ndi akatundu apa town. wamva? sungandiyende njomba iwe wachepa mwana wang'ono. ungonena kuti ndikugaiye inayake uisovere lerolo basi Oh? Wachepa iwe sungandiyende njunga ukuganiza ugapange zamsete umapanga ndi athu kumanena kuti iai ine kuno ku TNM pangani zakuti? eh! iweyo iwe ndi unjeni kapolo wa tauni ukufuna inayake basi. kugofotokoza kuti mayi zandivuta ndikozeni inayake ndigule sopo lero basi. kuti unjeni kunukhako kutani kusithe. osati ugalu ukundiuza apawu TNM wayamba ntchito ku TNM litilo wayamba liti? Ati chani? eh ndakuvanitu Iweyo ku TNM galu ngati iwe wayamba liti ntchito ku TNM iweyo? iwe shasha iweyo mwana wang'ono utifunse ife acheniwake azimenezi wamva? ndikhoza kukuphunzitsaso game mmene ungasewerere pa town pano kuti uzitorere wamva? mwati bwanji madamu? wachepa ameneyoyo mzakoyo wachepa ndikhozanso kumumphunzitsaso game yapatauni kuti atani, azitolerane. Eh kumafunikatu azimayi achocho ochangamuka ngati inuyo Eetu Adaa nanga awawa andiimbile amuyimbile mkazi wa patauni ozidziwa zonse Adaa! kundiuza kuti unjeni ife kuno ku TNM. unakagonena aisee lero zandivuta lelolo. shuga sopo kulibe ku deni. tiona zochita. Eh aa zoonadi madamu. Aise munthu waku TNM samaveka pachiphokoso ali pa chipwilikiti ngati uli ku unjeni uli ku unjeni uli ngati ku unjeni, unjeni kwa unjeni ku Ndilande kwa unjeni kwa Safalawo. Aaa aisee hahahaha Mumakhalira kuti mayi wanga? Eee? Mumakhalalira kuti mayi wanga? Iyayi sizouuzana kokhaliranso iai. basi Apapa tadziwanatu Eetu next time. akuluakulu pa tawuni akuluakulu pa tauni anthu tinachangamuka sikuberan kwake kumenekuku iai. sizingagwire olo ndi pang'ono. Tizidzutsana mawawu kuti muli bwanji mayi wanga, nnga bwanji kumeneko? Basi and mmene ukumvekera kumeneko sunavarenso mask soo. kolona ikuphansotu. sunavare mask iweyo. kumene ndilili kuno ndimalonderedwa ndi mfuti mayi wanga. sindigaphedwe iyayi. iyayi ndikunena ndikunena kolona. kolonatu ilibe mfuti aise. kolona ikupha virus ikuphatu. Ayi. tsono mayi wanga Eee Ndee ndiye mwati apa tizipanga bwanji? Iai ndiye ndikuimbila ndikuuze game yapa town osatu ugalu mukupanga ukufuna uziwabera athuwa iai wamva? ndikuimbira ineyo Okay Eee Muimbanso eti? Uwauze azako kuti ati tachepa awa ndi azikuluakulu apa town sitigawayende jomba. Ndi save nambalayi eti? Eee Ndiseve nambalayi? Zili kwa iwe. bola ukaiseva bola ukaisevapo usajuduke nayonso iai undisamale bho bho poti sukudziwa pomwe ndikuyakhulila ine hahahahahah chifukwa sukudziwa pomwe ndikuyakhulira ine iai. waona? Eee? Eee Ndiye mundipatse ya 9. ya 9 muli nayo? Ya 9 ndikupatsa nthawi ina yake bola ndapeza nambala yako aise. Okay Koma game iyiyi siyomawabera athu iyayi. tachepetsani moto pondani break basi Ayi tikuuzaaa ndikuuzaninso mochitila mwake mayi wanga. Iayi iwe sungandiuze mochitila. ine ndi amene ndigakuuze iweyo. Tiyakhulana bwinobwino Okay okay Yeah Sharp. zitani zimenezo aise sungandibere ine iai. achitsilutu awa ati kumanama kuti ndi waku TNM. chani chani chani zabodza. kufuna kundibera.
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_700.wav
30
60