audio
stringlengths
43
45
text
stringlengths
0
24.1k
start_time
int64
0
1.83k
end_time
float64
1.74
1.85k
./data/chichewa-dataset\audio\segment_301.wav
570
600
./data/chichewa-dataset\audio\segment_302.wav
600
630
./data/chichewa-dataset\audio\segment_303.wav
630
660
./data/chichewa-dataset\audio\segment_304.wav
660
690
./data/chichewa-dataset\audio\segment_305.wav
690
720
./data/chichewa-dataset\audio\segment_306.wav
720
750
./data/chichewa-dataset\audio\segment_307.wav
750
780
./data/chichewa-dataset\audio\segment_308.wav
780
810
./data/chichewa-dataset\audio\segment_309.wav
810
840
./data/chichewa-dataset\audio\segment_310.wav
840
870
./data/chichewa-dataset\audio\segment_311.wav
870
900
./data/chichewa-dataset\audio\segment_312.wav
900
930
./data/chichewa-dataset\audio\segment_313.wav
930
960
./data/chichewa-dataset\audio\segment_314.wav
960
990
./data/chichewa-dataset\audio\segment_315.wav
990
1,020
./data/chichewa-dataset\audio\segment_316.wav
1,020
1,050
./data/chichewa-dataset\audio\segment_317.wav
1,050
1,080
./data/chichewa-dataset\audio\segment_318.wav
1,080
1,110
./data/chichewa-dataset\audio\segment_319.wav
1,110
1,140
./data/chichewa-dataset\audio\segment_320.wav
1,140
1,170
./data/chichewa-dataset\audio\segment_321.wav
1,170
1,200
./data/chichewa-dataset\audio\segment_322.wav
1,200
1,230
./data/chichewa-dataset\audio\segment_323.wav
1,230
1,260
./data/chichewa-dataset\audio\segment_324.wav
1,260
1,290
./data/chichewa-dataset\audio\segment_325.wav
1,290
1,320
./data/chichewa-dataset\audio\segment_326.wav
1,320
1,350
./data/chichewa-dataset\audio\segment_327.wav
1,350
1,380
./data/chichewa-dataset\audio\segment_328.wav
1,380
1,410
./data/chichewa-dataset\audio\segment_329.wav
1,410
1,440
./data/chichewa-dataset\audio\segment_330.wav
1,440
1,470
./data/chichewa-dataset\audio\segment_331.wav
1,470
1,500
./data/chichewa-dataset\audio\segment_332.wav
1,500
1,530
./data/chichewa-dataset\audio\segment_333.wav
1,530
1,560
./data/chichewa-dataset\audio\segment_334.wav
1,560
1,590
./data/chichewa-dataset\audio\segment_335.wav
1,590
1,620
./data/chichewa-dataset\audio\segment_336.wav
1,620
1,650
./data/chichewa-dataset\audio\segment_337.wav
1,650
1,680
./data/chichewa-dataset\audio\segment_338.wav
1,680
1,710
./data/chichewa-dataset\audio\segment_339.wav
1,710
1,740
./data/chichewa-dataset\audio\segment_340.wav
1,740
1,770
./data/chichewa-dataset\audio\segment_341.wav
1,770
1,800
./data/chichewa-dataset\audio\segment_342.wav
1,800
1,824.158188
./data/chichewa-dataset\audio\segment_343.wav
TRANSCRIPT FOR DOWA ÐKAYEMBE Zikomo kwambiri amayi nonse. Zikomo. Funso lathu loyamba, tufuna tidziwe kuti kodi inuyo munatengapo mbali bwanji mu Project ya Care yomwe inali mu dela muno? Ineyo ngati number 4, tinatengapo mbali pa Care imeneyi, chifukwa, zimene imatiphunzitsa ngati kadyedwe, kadyedwe kabwino timayesetsa kuti tikwanilitse zimene akutiuzazo. Ena mbali yomwe munatenga ndi iti? A number 3, tinatengapo mbali yonena kuti atiphunzitsira amuna athu kuti adziwe Gender. Mmmh. Ine ngati Number 6, Project imeneyi yatiphunzitsa kuti mwana akangotentha thupi tidzithamangira ku chipatala. Ohoo. Ndithu. Ine Number 1. Project imeneyi yatithandiza kuti azimayi tidziwe kukhala mma gulu akubwereketsa ndi kusunga, moti ma gulu amenewa yatithandiza ngati ku mbali ya madyedwe, sizikutivuta chifukwa Ziweto zina, tudziwetela tokha kuchokera kumbali yochokera ku ma Bank Nkhonde, koma upangili onsewu, wachokera ku bungwe la Care, Zikomo. Mmmh Zikomo, Ena. Ine number five, Project imeneyi taphunzitsapo kadyedwe kabwino pa banja pathu. Mmmh, Zikomo.Ena. Ine number 2, Project imeneyi yatiphunzitsa zinthu za nkhani zoti sitimadziwa chifukwa kalero timangokhalilamo mchi mbulimbuli, ndipo anthu amanyela mkhuti, koma yatipatsa chiphunzitso, lero anthu alubiba mu vimbudzi, ngakhale ali wana adazolowela chikhalidwe chabwino ngati ku chisamalilo ngati chimenechi, chifukwa kale wanthunso amangobiba osasamba ndi mmanja momwe nkutani, kutulukamo, koma lero wanthu ali akusamba mmanja akachoka ku Chimbuzi kukhala ngati kuti chiyambi cha moyo wina oteteza matenda. Mmmh, zikomo kwambiri zikuonetsa kuti tonse tinatengapo gawo mbali zosiyasina siyana mu Project imeneyiyi ya CARE. Nanga pa zaka zitatu zimenezizi Project imeneyiyi imagwira ntchito, zilipo zina zomwe inuyo mmaona kuti zasintha kumbali ya kadyedwe kabwino, ngakhalenso maudindo amene amakhala nawo pakati pa amayi ndi abambo, mukuona kuti chasintha ndi chani? Ine number 1. Project imeneyi pa zaka zitatu zimenezi zasintha nzambiri zina mwa izo, kale maudindo amangoima na azibambo okha okha, koma panopa ngakhale mzimayi aluimila Chair ku ADC, Chair kumudzi, ma VDC osiyanasiyana, moti pamene ndukamba pano ineyo ndine Chair wa VDC Komanso Member wa ADC, zikomo. Aaah zosangalatsa, ena. Chilipo china chilichonse chasintha mu zaka zitatu zimenezi kumbali ya maudindo ngakhalenso kadyedwe kabwino? Ine ngati number 6, Pa zaka zitatu zimenezi zosintha ndi zambiridi. Chifukwa chonena kuti ife pabanja pathu sitimadziwa kuti wina akatangwanidwa mamunanso amaphika. Ndiye kuonetsa kuti zatiphunzitsanso kumbali ya Gender, tuthandizana ntchito za pakhomo, zikomo. Ine number 3, kumbali ya Gender yomweyo. Zatiphunzitsanzo kuti tikapeza ndalama mnyumba muja amayi adzikhalakonso ndi mbali, munthu wammunanso adzikhala ndi mbali kuganiza maganizo pamodzi kuti kodi titani ndlama tapeza izi. Zikomo. Zikomo.Ena. Ine ngati number 4, moonjezela momwe anzanga anenelamo poti yasintha ndithu zinthu zochuluka. Project imeneyiyi yatisintha ku madyedwe, moti kalelo sitimadziwa kuti kodi zakudyazi, timadyelamo, zoti zili ndi magulu sitimadziwa ndiye panopa tadziwa ndondomeko yonse ya kadyedwe koyenela. Panopa wana wathu ndi wa thanzi, ifeyo timanchitilamo, komanso wana wa nzeru. Panopa tere wonena kuti akupita ku sukulu mwana wa nzeru ndithu, zonena kuti mwana akamapanda kudya zakudya zakasinthasintha amakhala mbuli sitimazidziwa nga si tidali mchimbulimbuli, koma panopa tili ndi wana wa nzeru komanso makomo ya thanzi zedi. Ine ndine Number 2. Bungwe ngati limeneli lationetsa moyo wamakono, pamene kale tidali mchimbulimbuli. Yasintha zinthu Zankhani. Kale madzi timamwa pa vithaphwi, koma lero ukayamba kuyenda umaona kuti timijigo imapezeka ndithu ngakhale midzi ina idakalibe, koma aah aah yasintha kwa kukulu kutsata ngati nkhani ya za umoyo ngati imeneyi yatiyangÕanilako ndithu, chifukwa kale kumakhala kumadwala ma Cholera, koma lero Cholera yo ali kumveka koma cha dela la kutali kuno kwathu kuno ayi zikuonetsa kuti zathandizako ndithu; monga ngati nkhani ya matenda ngati yotsegula mmimba, ayi kukhala ngati mbiri yakale. Lero lino zidakhala ngati zidasinthako ndithu. Bungwe limeneli latisamalila motero. Ine Number five .Bungwe limeneli latithandizila kuti, bungwe limeneli latithandizila kuti mmakomo mukhale ukhondo, moti mmakomomu mudasintha chifukwa cha bungwe limeneli zikomo. Chiliponso china chomwe taona kuti chasintha mu zaka zitatu zimenezi? Talongosolako ku mbali ya Ukhondo, talongosolako nkhani ya kadyedwe kabwino, talongosolako nkhani ya maudindo kuti kale abambo ndi amene amakhala ndi maudindo akuluakulu okha amayi ayi, china chomwe taona kuti mu zaka zitatu zimenezi chasintha ndi chani, mwina mongoonjezela. Ine ndine Number 2. Monga ngati pa gawo limeneli kalelodi maudindo amangokhala ndi anthu amuna okhaokha, koma tidaona kuti labwera ngati bungwe limeneli lero zinthu zidasintha zedi, kumatheka mzimayi kutsogolerama ma gulu ya anthu amunawa, kusonyeza kuti Gender pamenepapa idatani, idagwira ntchito zedi, zikomo. Ena tili ndi ndemanga Ina yokhuzana ndi kusintha kumeneku mwina mongoonjezela? Mongoonjezela tili pa kadyedwe pomwepo ku mbali ya mwana tsopano. Kale zoti mwana akabadwa aluyenela kuti aziyamwa mwakathithi sitimadziwa, timangoyamwitsa apo tafunila, mwina ayamwa mmawamu lonseli ilili, osayamwa mwana mwina udzimuyamwitsa cha mma 4, koma panopa adatizindikilitsa, panopa mwana akangobadwa tumuyamwitsa mwa kathithi. Zikomo. Number 1. Mawu oonjezelaponso pangÕono, kale mwa zikhulupiliro omati mzimayi oyembekezela asadye dzila, koma litabwera bungwe limeneli aah zonse tidadzitaya, mzimayi oyembekezela akudya dzila bwinobwino chifukwa lili ndi ntchito yakenso mwa nzimayi oyembekezela. Panopa akumachila bwinobwino pamene kale Amati mwanana akabadwa wadazi, koma panopa zinthu zasintha kuno kwathu, mzimayi oyembekezela Ali kudya china chilichonse chimene chidali mzikhulupiliro kale. Zikomo. Ine ngati Number 6. Mongochitira ndemanga zimene akamba amayi awa, Kale azimayi oyembekezela amakonda kuchilila kunyumba, koma pano momwe lidangoti labwera bungwe ili simungamvepo mzimayi wachilila panjira kapena kunyumba, azimayi tikuthamangila ku chipatala kukakhala chidikilo kapena kuona kuti aah lero ndamdzuka bwino, kuthamangila ku chipatala kuti ukathandizidwe, ndiye bungwe limeneli latithandiza kuti azimayi adzithamangira nsanga ku chipatala akakhala oyembekezela, zikomo. Mmmh. Ine ndine a Number 3. Kuthilanso ndemanga pa mawu amene akamba awa, zonena kuti za chikhu, za vikhulupiliro, bungwe limeneli latiphunzitsa kuti zithe. Chifukwa chonena kuti amanena kuti kuti munthu asadye nthochi zobatana akaona mapasa, koma pano ali kudya munthu nthochi zobatana mapasa saliuona, zikomo. Mmmh. Ine ndine number five. Bungwe limeneli latithandiza kuti mmakomo mwathu tidzikhala athanzi, tidzigwira ntchito zodalilika chifukwa matenda satipeza pafupipafupi zikomo. Mmmh. Kodi mukuona kusinthaku kwachitika chifukwa chani, mu zaka zimenezi kuti muthe kudziwa zinthu zina momwe mwalongosoleramo, chapangitsa kusinthako ndi chani? Ine ndine Number 1. Chapangitsa kuti mmakomo mwathu tisinthe ndi upangili ochokera ku bungwe la Care, chifukwa kale mmbuyomu zimatheka ndithu timangochitapo, koma litabwera bungwe limeneli latithandiza kuti mmakomo mwathu tisinthe, zikomo. Ine ngati number 6. Mongoonjezela pa zaka zitatu zimenezi chaoneka kusintha kwambiri chifukwa cha bungwe limeneli chifukwa choti kale mabungwe ngati awa kudalibe, ndiye apapa zapangitsa kuti zikhalenso ngati zinthu zatsopano, Zikomo. Ndiyeno, mwina mu zaka zitatu zimenezizi, chiliponso chinthu china chomwe tikuona sichinasinthe. Chomwe sichinasinthe ndi chani? Ine ndine Number 1. China chimene tikuona kuti mu zaka zitatu zimenezi sichidasinthe, ndi mavuto amene timakumana nawo pa ulimi, mwina tikhonza kulima mbewu, mbewuzo zikumana ndi tizilombo tinatake, mbewu zija nkuuma.Ndiye kuti pamene paja madyedwe abwino ali kukalephera, zikomo. Zikomo, ena.Chomwe tikuona kuti sichinasinthe changokhala chimodzimodzi mu zaka zitatu zimenzi ndi chani? Ine ndi Number 2.Mu zaka zitatu zimenezi icho tuona kuti sichinasinthe, mwina kukhonza kutheka munthu ukakololapo, mbewu ija ikapita kunsika mwina sikukayenda malonda bwino yayi, ndiye mwina zachuma zimakhalanso kuti zatani, zavutavuta, ndiye kuti mwina madyedwe onena kuti uphatikizille mchisAmaliro cha ndalama chimakhala kuti chikutaninso, chikuvutanso pamenepopo. Mmmh. Zedi mongothilira ndemanga, ine ndine Number 6. Mmene akambila amayi awa ndi zedi. Kulima timalima ndithu zedi, koma kuti tipeze phindu lochuluka kuchokera ku ulimi kuli utivuta, chifukwa choti mitengo Sali kutipatsa yabwino, ndiye kuti tionjezele zina zokhudzana ndi madyedwe abwino, chifukwa pali ngati kuti ukagule mafuta uthile ku ndiwo zimakhala kuti waTEnga chani ndlama, ndiye ndalama zimenezo zikutisowa, zikomo. Zikomo. Chabwino, aah mwalongosola zinthu zimenezizi, ndi mavuto anji amene mwina mmanyumbamu mmudzi munomo mwakhala mukumana nawo okhudzana ndi kadyedwe koyenela, amene chakupangitsanikuti mwina musafikile kadyedwe koyenelako. Musakwanilitse. Ine ndine Number 1. Mavuto amene tukumana nawo kwambiri ndi mavuto osoweka chakudyawa, kusowa chakudya, kusowa zipangizo zokagulira zinthu zimene zonena kuti tikhonza kukwanilitsa pa madyedwe abwino. Mmmh. Ena ndi mavuto otani amene takumana nawo amene takumana nawo akuti akumatilepheletsa kuti tifikile kadyedwe kabwinoka Ine ndine number 2. Madyedwe abwinowo amavuta, mwina ukalima mbewu ija ikakukanika ndlama ulibenso, ndiye kuti ukwanilitse madyedwe amene aja, amakhala kuti akuvutavuta, ndiyee mwina thandizo lina linanso limakhala kuti lakusoweka kuti ulipeze. Mmmh. Zedi. Ine number 4. Mongoonjezela pomwepo mavuto ake amavuta ndithu ndi mbali ya ulimiyi, chifukwa utha kulima walima mbewu zija zosiyana siyana nyemba walimako, chimanga walimako, fodya walimako, ndiye umapezeka kuti mwina nyemba ukolola, ndiye kuti ngati za masamba izi sizovuta, timadzala pomwe pakhomo, bwinobwino, koma tsano chimene chimadzavuta mwina ngati timbeuto wapita nato kunsika ngati fodya uyo ngati chimanga kuona kuti timitengo tosayenelela ndi mmene akugulira, ndiye zimapangitsa kuti ka ndalamako, koti ukawonjezele pa iti wakololati, kuti ukagule timafuta, zimakhala kuti zuta zuvuta,kuonjezela madyedwe aja, zedi. Zikomo. Aliponso ena amene ali ndi ndemanga mwina pa mavuto omwe timakumana nawo mmudzi ngakhalenso mmanyumba mwathu amene akutilepheletsa kuti mwina tifikile kadyedwe kabwinoko? Ine ndine number 2. Monga ngati kutengela gawo la okalamba. Okalambanso nawo amakhala onena kuti, nkhani ya kusowa kwa thandizo kwa iwe woonekako woti amadandaulitsanso zedi, amakhala ngati awa okalambawa chifukwa chonena kuti mafuta enieniwa sawadziwayi, chifukwa cha gawo la zomwe tunena ndithu cha vuto la za chuma ndi kutsika kwa mitengo, kwa zithu ntero tee. Ine ngati number 6, mongoonjezera ndi mmene akambira amayi awa ndi zedi kumbali nanga muja tidabwera ndi azipongozi aja eti wonena kuti thandizo lambiri moti timachita kuwapatsako, ndiye zikakhala kuti iwe zakuvuta, iwo aja zimakhala zawavuta, iwo aja pakali panopa alibe kena kalikonse kamene kakuwathandiza, akuona kwa ife ana.Ndiye kumapezeka kuti ife tili kutenga tili kuwapatsa zathunso zuchepa, ndiye Kamba kopatsana kuja pamakhala kuti mavuto alowa makomo onse awiri, tonse timakhala kuti tsano nthawi ina tilibe chilichonse chonena kuti tikhonza kutani kukwanilitsa, zikomo. Zikomo kwambiri, Aliponso ali nde ndemanga pa nkhani imeneyi? Tsano poti ife tabweretsa ana? Eee nkhani imene tukambirana inali ya mavuto omwe mwina timakumana nawo mmanyumbamu, mwina amene akutilepheretsa kuti tifikile kadyedwe kabwino, ndi mavuto anji? Ine number five. Mavuto onena kuti munthu pabanjapo takolola zochepa ndiye kuti ukwanilitse kudya za magulu angapo, zimavuta. Mapeto ake umakantengapo chinthu chimodzi pa tsikulo basi. Ndiye mwina, ndingomva maganizo anu, chomwe chingapangitse kuti mwina tidzitha kudzala mbewu zoti zisavute nsika tinayamba taganizilapo kuti pali mbewu zina zomwe mwina titha kugulitsa mosavuta zoti mwina zimakhalako ndi ntengo wokwera kuti mwina tizidzala zimenezo? Ine ndine a Number 3, Monga ngati kuno tidazolowela kulima fodya ndi Soya ndiye sitingadziwe kuti kodi inu mukhonza kutipatsa maganizo oti mudzilima mbewu yakuti kuti mudzionako kuti mudzipezako phindu. Ine ndine Number 1. Mbewu zina timalima, zodalira ngati kuti zizikhala ngati zizitithandizila ngati chimanga chitachepa, tidzikhala ndi mbatatesi, mbatata, ndiye mbatata izi sikuti timagulananso mokwera mitengo pazifukwa zoti zimangokhala khomo ndi khomo tsano, ndiye timangogulana kaya tiuugulana kani chani, ndiye zimativuta. Ndiye mbatata ija si mwina sisowa timangodya ngati basi nsima takhuta, basi, koma osati tigulitsane kuti ntengo ukwelelepo, ayi. Nanga si a Neba ndi a Neba. Aaa ndakumvetsetsani, nkhani zake zimakhala zonena kuti mbewu zambiridi, zimakhala zoti aliyense walimako, ndiye umakhala ngatidi wavuta. Chabwino. Nanga tudziwa chani zokhudzamna ndi kadyedwe kabwino? Kodi kadyedwe kabwino kamatanthauza chani? Mwina mongokumbutsana tisanapite mafunso enawo.Mau oti kadyedwe kabwino. Ine ndine number 1. Mau onena kuti kadyedwe kabwino, zikutanthauza kuti pa tsiku, munthu adzidya zonse za magulu sikisi. Koma chifukwa cha mavuto amene tafotokozawa, pena timakwanilitsa, koma masiku ena sititani, sitimakwanilitsa. Zikomo. Ine ngati Number 6. Mawu yoti kadyedwe kabwino, akutanthauza kuti tidzidyako zakudya za magulu sikisi, Kaya tapezako zitatu, tikhala ngati ndithu tatengako ndithu mbali pamenepo. Chifukwa nthawi zina sitingakwanilitse zonse sikisi kuzipeza ndi mavuto amene tili nawo. Koma tidzidyako zitatu, ndiye kuti pakhomo pathu pakhala pa thanzi. Mmmh. Aliponso ena mwina nagaonjezele kadyedwe kabwino. Mongoonjezela, ine number 4, kadyedwe kabwino mmene ndimamvetsetsela ndi zakudya za magulu omse sikisi. Ndiye magulu amenewa muja tanenela kuti alipo sikisi, ndiye amafunika kuti munthu adzikhala kuti magulu onsewa wakwanilitsa pa tsiku. Ndiye momwe anenenela kuti poti timakhala kuti tapeleweledwa, sitikukwanila, timayesetsa ndithu kuti patsikupo udzikhala kuti magulu atatu kapena folo udzikhala kuti wayesetsa kuti wataniko ndithu, wadyako. Owo zikomo kwambiri. Mongokumbutsana kadyedwe kabwino kakukamba momwe mwanenela zakudya za magulu onse sikisi, kaya tidyako atatu koma utengepo gawo pa maguluwo. Utha kupezeka masana wadya atatu, kaya nthawi ina wadyako konso ina, ndiye magulu aja amakwana. Komanso zukamba zokhudzana ndi zakudya zimene zamagulu, maganizo omwe timapanga pogula ndi kugulitsa, zinthu ngati zokhudzana ndi zakudya, kasungidwe ka chakudya, zukamba momwe tinga, za ulimi, kuyamwitsa ana, kupita kuchipatala pamene tadwala kapenanso ndi ana, ukhondo wa pakhomo okhudzana ndi madzi kapenanso pamene tutengapo mbala kaya pa za kapangidwe ka ziganizo mnyumba pakati pa abambo ndi amayi, eeh, ndiye kadyedwe kabwino kakumangilila zinthu zomnse zomwe timachita zimakhudzana ndi kumbali ya chakudya,mmh. Madzi omwewa momwe mungawasamalilile mukatunga ndimkadyedwenso kabwino kameneko, chifukwa ngati simunatunge madzi abwino olo zomwe mutakaphike kunyumba sidzikhalanso bwino, Zikomo kwambiri. Pali nthawi inoyi timafuna tidziwe, kuti kodi tikati nkazi wabwino, amene mumafuna atakhala choncho, nkazi wabwino akuyenela kupanga zinthu zitizo mbali ya kadyedwe kabwino ngati tatchulaka, nkazi wabwino, akuyenela kupanga ngati zitizo, ntchito zitizo zomwe nkazi wabwino akuyeneka kupanga ku nkhani ya kadyedwe kabwino? Ineyo ndine number 1. Nkazi wabwino, mmawa atadzuka ayenela ayambe watenga chisesa asese pakhomo, zilizonse chikhale chonzekela kuti lero li ndipanga chakudya, ndiye nkazi wabwino. Mmmh. Zikomo. Ine ndine Number 2. Nkazi wabwino amati kukacha mmawa asese pakhomo, akasesa pakhomo apite kudambo, kenaka aone wana kuti kodii wana akudya chani popita ku sukulu, ngati mmawa umo, ndiye pakuphatikiza kuti kapena anawa apita ndiye umaona kuti tsono ndione za ndiwo ndiphika chani, basi ndaima pomweppo. Ena. Nkazi wabwino ku mbali ya kadyedwe kabwino kaya Ine ndine number 6. Nkazi wabwino kumbali ya madyedwe ndiye kuti amafunika mmawa kukacha, atenge chisheda ashede pakhomo, atsuketsuke tsuke ziwiya zonse akonze chakudya choti wana adye popita ku sukulu, kenaka aone kuti wamuna akachoka ku ntchito adzadya chani. Wamuna aja adzidzapeza tson nsima wawaphikira, timadzi tili pafupi, ndiye munthu uja amatchedwa nkazi wabwino. Mmmh. Aliponso amene afuna kuonjezela? Aaah zoonjezela zake zikhonza kukhala zomwezo. Owo, zikomo. Nanga mamuna wabwino, kuti mamuna wangayi ndi mamuna wabwino, kapena ndimafuna atakhala wabwino chonchi kumbali ya kadyedwe kabwino kapakhomo akuyenela kupanga chani? Ine ndi Number 3. Mamuna wabwino ndi amene Amati kutacha mmawa kupanga pologalamu yoti lero akazi wanga, tidyeko kanyama aka, tidyeko kasinthakasintha, zikomo. Ine number 4. Ine ndikuona kuti mamuna wabwino, ndi amene amakhala kuti akugwira ntchito pakhomopo moganizila, moganizilana ndi nzake ngati nkazi wake, komanso ngati kumbali ya madyedweyi ndiye kuti mukhale onena kuti iyeyo ali kukwanitsa kumbali ya zipangizo, ndiye kutinso pamenepa pakukapezeka kunena kuti mamuna ameneyu ndiye kuti chilichonse mudzithandizilana pakhomo paja ngati kumbali ya ntchito tsano, komanso maganizo mudzikhala oti mudzipatsana maganizo pochita chinthucho, eya.Ngati ku mbali ya ndalamayo mwina mwadzuka, aaah amayi apa titani, mwina mmawa muja mwashedasheda aah amayi aapa titani, mwina iwo akukatunga madzi iwe uli kusheda, ndiye kuti abwerako aah aah ndiye kuti mmene kulilimu nanga si mwana chakudya cha mmawa adzipita ku sukulu, aah aah ndiye kuti ka ndalama kaja tantengamponi mukatani mukagule ngati nti sikono mwana adye adzipita ku sukulu, pamene paja ndiye kuti mupatsana maganizo. Osati mamuna uja apange yekha kapena nkazi apange yekha aah aah, ndiye kuti mamuna wabwino ayenela kukhala otereyo. Oho, zikomo.Inuyo ngati mayi wapabanjapo ngati nkazi, ndi udindo wanu wanji, udindo wanu ndi wanji pa nkhani ya kadyedwe kabwino kutengela mukadzuka mmamawa, muli ndi udindo wanji ngati mayi? Mutakonza chakudya? Kumbali ya kadyedwe kabwino, kukacha mmamawa udinndo wanu ndi wotani ngati mayi wapabanjapo? Ine ndine number 3. Udindo wa mayi kutacha mmawa, amayenela aphike pha, aphike chakudya kuti anthu ali pamenepo adye, monga ngati phala madyedwe abwino. Mmmh. Ine ngati number 6. Udindo wa mayi ngati mamuna uja wakukonzera chakudya, kuti chakudya chija chikhale chaukhondo chimafunika iwe mzimayi. Mmh. Ngati ugwiritsa ntchito ziwiya zosatsuka, amuna akupangila china chilichonse ndiye kuti madyedwe ake abwino pamenepo yatani, yavuta. Chifukwa sungatenge chakudya chabwino kuika mu mbale zosatsuka. Ndiye pamenepo udindo waukulu uli ndi mayi chifukwa chonena kuti amafunika alongosole katundu yense amene amagwiritsa ntchito akhale oyela, zikomo. Zikomo. Ine number five. Ndamanga ya mayi awo, mayi atadzuka mmawa adziyamba kukonza ziwiya zonse, kenako aphitse madzi awapatse abambo aja, kenako akonze chakudya adye, zikomo. Mmmh. Ineyo ndine number 1.mongoonjezela, udindo wa mayi ameneyi ayenela akhalenso wa ukhondo, aziwonanso anawa kuti pakhomo akuona bwanji, kapena ineyo pamene ndukonza chakudya nduoneka bwanji, zikomo. Ndiye tsiku, momwe kwachela tsiku ndi tsiku kukacha ngati ifeyo azimayi, timapanga chani, zokhudzana ndi kadyedwe kabwino, kukacha mmamawa muja, timapanga zinthu ziti? Ine ndine number 1. Mmawa kutacha, munthune ndimapanga business ya tomato, ndimayenela nditengeko tomatoyo ndiwasiile ana, ndisiyenso chakudya akonza abambo muphike, ndiye kuti pamene ndizichoka pakhomo paja ndiyesetsa kuti pakhomo paja chilichonse chatani, chayenda. Ndikabwerako ndiyenela ndimulandire uja ndipangenso chakudya ndine, kuti pakhomo ziyende. Owo, zikomo. Ena tsiku ndi tsiku ngati mayi wapakhomo timapanga ntchito zitizo zokhudzana ndi kadyedwe kabwino timatani, mwina mongonjezela? Ine ngati Number 6, Enafe tili ndi manyumba yokhula, ndiye ngati mayi wa pakhomo umakonza kuti Owo mwezi watha ndidakhula, mnyumba mwangamu mwezi watha ndidakonza mnyumba mwangamu pano simuli bwino, fumbi. Chifukwa mwina zikhonza kutheka watsukatsuka mbalezo, uli usesa monga pakhomo fumbi PHA PHA pha, ndiye kuti fumbi lonse lija lupitanso kuti, ku katundu uja wasamala uja, ndiye madyedwe abwino amafunika udziyambanso kukhula kenako zinazo zizikhalanso mmalo mwake, zikomo. Zikomo. Ena tili ndi maganizonso ena oonjezela/ Ineyo number 4. Mzimayi akadzuka mmamawa, udzuka ndiye kuti usheda sheda pakhomo paja, ndiye kuti mkhitchini ushedasheda kuwaza timadzi tako, ndiye kuti upitanso ku toilet kuja ukapsedepsede kuwaza timadzi, kenako uwone kuti kodi madzi alimo osamba mmanja.Ndiye kuti ngati mulibe utenga utsuketsuke mmene muja uthilemonso ena, tsiku lililonse ukhale kuti mudzikhala madzi ena, osati adzulo apezane ndi a lero, zikomo. Mmmh. Nanga abambo ali ndi udindo wanji mmh, pankhani ya kadyedwe kabwino kapakhomo, abambo udindo wawo dniwotani? Ine ndine number 2. Mmmh. Abambo udindo ali nawo, chifukwa chonena kuti kukhonza kutheka kutangwanika, koma abambo amataninso, amatha kugwira ntchito ina ija, kuti nonse mutani mudye ndithu. Ngakhale kuli kusokola zinthu ndiyenso ali ndi udindo wa Number 1 abambo. Ndiye kuti amatenga ndalama kukagula chinthu chija kubwera nacho pakhomo paja kuti madyedwe abwinowo akhale natani, nalongosoka. Mmmh. Inde, kumakhala kukambirana mu umodzi umenewo kuti lero, kutuluka ndlama mwakuti yokagula chakutichakuti chotere. Tikonze madyedwe abwino ya pakhomo pano. Zikomo, ena. Abambo. Abambo ali ndi udindo wanji? Ine number five. Abambo amatengaponso gawo losokola zinthu pa tsiku limenelo, kuti banja lawo lidye, zikomo.
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_344.wav
30
60
./data/chichewa-dataset\audio\segment_345.wav
60
90
./data/chichewa-dataset\audio\segment_346.wav
90
120
./data/chichewa-dataset\audio\segment_347.wav
120
150
./data/chichewa-dataset\audio\segment_348.wav
150
180
./data/chichewa-dataset\audio\segment_349.wav
180
210
./data/chichewa-dataset\audio\segment_350.wav
210
240
./data/chichewa-dataset\audio\segment_351.wav
240
270
./data/chichewa-dataset\audio\segment_352.wav
270
300
./data/chichewa-dataset\audio\segment_353.wav
300
330
./data/chichewa-dataset\audio\segment_354.wav
330
360
./data/chichewa-dataset\audio\segment_355.wav
360
390
./data/chichewa-dataset\audio\segment_356.wav
390
420
./data/chichewa-dataset\audio\segment_357.wav
420
450
./data/chichewa-dataset\audio\segment_358.wav
450
480
./data/chichewa-dataset\audio\segment_359.wav
480
510
./data/chichewa-dataset\audio\segment_360.wav
510
540
./data/chichewa-dataset\audio\segment_361.wav
540
570
./data/chichewa-dataset\audio\segment_362.wav
570
600
./data/chichewa-dataset\audio\segment_363.wav
600
630
./data/chichewa-dataset\audio\segment_364.wav
630
660
./data/chichewa-dataset\audio\segment_365.wav
660
690
./data/chichewa-dataset\audio\segment_366.wav
690
720
./data/chichewa-dataset\audio\segment_367.wav
720
750
./data/chichewa-dataset\audio\segment_368.wav
750
780
./data/chichewa-dataset\audio\segment_369.wav
780
810
./data/chichewa-dataset\audio\segment_370.wav
810
840
./data/chichewa-dataset\audio\segment_371.wav
840
870
./data/chichewa-dataset\audio\segment_372.wav
870
900
./data/chichewa-dataset\audio\segment_373.wav
900
930
./data/chichewa-dataset\audio\segment_374.wav
930
960
./data/chichewa-dataset\audio\segment_375.wav
960
990
./data/chichewa-dataset\audio\segment_376.wav
990
1,020
./data/chichewa-dataset\audio\segment_377.wav
1,020
1,050
./data/chichewa-dataset\audio\segment_378.wav
1,050
1,080
./data/chichewa-dataset\audio\segment_379.wav
1,080
1,110
./data/chichewa-dataset\audio\segment_380.wav
1,110
1,140
./data/chichewa-dataset\audio\segment_381.wav
1,140
1,170
./data/chichewa-dataset\audio\segment_382.wav
1,170
1,200
./data/chichewa-dataset\audio\segment_383.wav
1,200
1,230
./data/chichewa-dataset\audio\segment_384.wav
1,230
1,260
./data/chichewa-dataset\audio\segment_385.wav
1,260
1,290
./data/chichewa-dataset\audio\segment_386.wav
1,290
1,320
./data/chichewa-dataset\audio\segment_387.wav
1,320
1,350
./data/chichewa-dataset\audio\segment_388.wav
1,350
1,380
./data/chichewa-dataset\audio\segment_389.wav
1,380
1,410
./data/chichewa-dataset\audio\segment_390.wav
1,410
1,440
./data/chichewa-dataset\audio\segment_391.wav
1,440
1,470
./data/chichewa-dataset\audio\segment_392.wav
1,470
1,500
./data/chichewa-dataset\audio\segment_393.wav
1,500
1,530
./data/chichewa-dataset\audio\segment_394.wav
1,530
1,560
./data/chichewa-dataset\audio\segment_395.wav
1,560
1,590
./data/chichewa-dataset\audio\segment_396.wav
1,590
1,620
./data/chichewa-dataset\audio\segment_397.wav
1,620
1,650
./data/chichewa-dataset\audio\segment_398.wav
1,650
1,680
./data/chichewa-dataset\audio\segment_399.wav
1,680
1,710
./data/chichewa-dataset\audio\segment_400.wav
1,710
1,740